
Chimwemwe mtsaya, Flames yapantha South Africa
Timu ya mpira wa miyendo ya Malawi the Flames’ yaswa timu ya South Africa ndi chigoli chimodzi kwa duu pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe. Masewelo a mu gawo lachiwiri (Round 2 ) ya African Nations Championship CHAN Malawi yamwemwetera mu chigoli …